Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 8:16 - Buku Lopatulika

16 Tulukamoni m'chingalawamo, iwe ndi ana ako, ndi mkazi wako, ndi akazi a ana ako pamodzi ndi iwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Tulukamoni m'chingalawamo, iwe ndi ana ako, ndi mkazi wako, ndi akazi a ana ako pamodzi ndi iwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 “Iwe ndi mkazi wako, ana ako pamodzi ndi akazi ao, tulukani m'chombomo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 “Iwe, mkazi wako, ana ako pamodzi ndi akazi awo tulukani mʼchombomo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 8:16
14 Mawu Ofanana  

Ndipo anati Yehova kwa Nowa, Talowani, iwe ndi akunyumba ako onse m'chingalawamo; chifukwa ndakuona iwe kuti uli wolungama pamaso panga m'mbadwo uno.


Tsiku lomwelo analowa m'chingalawamo Nowa, ndi Semu, ndi Hamu, ndi Yafeti, ana a Nowa, ndi mkazi wake wa Nowa, ndi akazi atatu a ana ake pamodzi nao:


Ndipo analowa Nowa ndi ana ake ndi mkazi wake ndi akazi a ana ake m'chingalawamo, chifukwa cha madzi a chigumula.


Mulungu ndipo ananena kwa Nowa, kuti,


Tulutsa pamodzi ndi iwe zamoyo zonse zili ndi iwe za nyama zonse, zouluka, ndi zinyama, ndi zokwawa zonse zakukwawa padziko lapansi; kuti ziswane padziko lapansi, zibalane, zichuluke padziko lapansi.


Yehova adzasungira kutuluka kwako ndi kulowa kwako, kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.


Pakuti adzalamulira angelo ake za iwe, akusunge m'njira zako zonse.


Iwenso, chifukwa cha mwazi wa pangano lako ndinatulutsa andende ako m'dzenje m'mene mulibe madzi.


Ndipo ansembe akulisenza likasa la chipangano la Yehova, anaima pouma pakati pa Yordani, ndi Aisraele onse anaoloka pouma mpaka mtundu wonse unatha kuoloka Yordani.


Pakuti ansembe akusenza likasa anaima pakati pa Yordani, mpaka zitatha zonse Yehova adazilamulira Yoswa anene kwa anthu, monga mwa zonse Mose adalamulira Yoswa; ndipo anthu anafulumira kuoloka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa