Genesis 7:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mvula inali padziko lapansi masiku makumi anai usana ndi usiku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mvula inali pa dziko lapansi masiku makumi anai usana ndi usiku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Choncho mvula idagwa pa dziko lapansi masiku makumi anai, usana ndi usiku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo mvula inagwa pa dziko lapansi masiku makumi anayi usana ndi usiku. Onani mutuwo |