Genesis 50:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo anakwera pamodzi ndi iye magaleta ndi apakavalo; ndipo panali khamu lalikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo anakwera pamodzi ndi iye magaleta ndi apakavalo; ndipo panali khamu lalikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Asilikali okwera pa magaleta ndi akavalo, nawonso adamperekeza. Motero chinali chinamtindi cha anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Asilikali okwera pa magaleta ndi asilikali a pa akavalo anapita nayenso pamodzi. Linali gulu lalikulu. Onani mutuwo |