Genesis 5:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Lameki anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala mwana wamwamuna; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Lameki anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala mwana wamwamuna; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Lameki ali wa zaka 182, adabereka mwana, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Pamene Lameki anali ndi zaka 182, anabereka mwana wamwamuna. Onani mutuwo |