Genesis 5:23 - Buku Lopatulika23 masiku ake onse a Enoki anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 masiku ake onse a Enoki anali mazana atatu kudza makumi asanu ndi limodzi ndi zisanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Adamwalira ali wa zaka 365. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Zaka zonse za Enoki zinali 365. Onani mutuwo |