Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 49:30 - Buku Lopatulika

30 m'phanga lili m'munda wa Makipela, umene uli patsogolo pa Mamure, m'dziko la Kanani, limene Abrahamu analigula kwa Efuroni Muhiti pamodzi ndi munda, likhale poikira pake:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 m'phanga lili m'munda wa Makipela, umene uli patsogolo pa Mamure, m'dziko la Kanani, limene Abrahamu analigula kwa Efuroni Muhiti pamodzi ndi munda, likhale poikira pake:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Lili kuvuma kwa Mamure m'dziko la Kanani. Abrahamu adaagula phangalo pamodzi ndi munda womwe kwa Efuroni Muhiti, kuti pakhale manda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Ili ndi phanga la mʼmunda wa Makipela, pafupi ndi Mamre mʼdziko la Kanaani. Abrahamu anagula phangalo pamodzi ndi munda womwe kwa Efroni Mhiti kuti pakhale manda.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 49:30
6 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Hiti analimbitsira Abrahamu munda, ndi phanga lili m'menemo, likhale lake lamanda.


Ndipo Abrahamu anauka pa wakufa wake, nanena kwa ana a Hiti, nati,


Ine ndine mlendo wakukhala ndi inu: mundipatse ndikhale ndi manda pamodzi ndi inu, kuti ndiike wakufa wanga ndisamthirenso maso.


Ndipo ana ake Isaki ndi Ismaele anamuika iye m'phanga la Makipela, m'munda wa Efuroni mwana wake wa Zohari Muhiti, umene uli patsogolo pa Mamure;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa