Genesis 48:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Israele anayang'ana ana aamuna a Yosefe, nati, Ndani awa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Israele anayang'ana ana amuna a Yosefe, nati, Ndani awa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Yakobe ataona ana a Yosefe, adafunsa kuti, “Nanga anyamata aŵa nga yani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Israeli ataona ana a Yosefe anafunsa kuti, “Anyamatawa ndi a yani?” Onani mutuwo |