Genesis 48:6 - Buku Lopatulika6 Koma obala iwe udzawabala pambuyo pao, ndiwo ako; awatche dzina la abale ao m'cholowa chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma obala iwe udzawabala pambuyo pao, ndiwo ako; awatche dzina la abale ao m'cholowa chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma obadwa pambuyo pa iwowo, ndi ako amenewo. Adzalandira choloŵa chao pamodzi ndi achibale ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Koma amene ati adzabadwe pambuyo pa iwowa adzakhala ako ndipo cholowa chawo chidzadziwika ndi mayina a abale awo. Onani mutuwo |