Genesis 47:21 - Buku Lopatulika21 Tsono anthu, anasunthira iwo kumizinda kuchokera kumphepete kwa malire a Ejipito kufikira kumphepete kwina kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Tsono anthu, anasunthira iwo kumidzi kuchokera kumphepete kwa malire a Ejipito kufikira kumphepete kwina kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Yosefe adaŵasandutsa akapolo anthuwo ponseponse m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 ndipo Yosefe anawasandutsa anthu onse kukhala akapolo a Farao, kuchokera ku malire a mbali ina ya Igupto kukafika ku malire a mbali ina ya dzikolo. Onani mutuwo |