Genesis 47:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo mwa abale ake anatengako anthu asanu, nawaonetsa iwo kwa Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo mwa abale ake anatengako anthu asanu, nawaonetsa iwo kwa Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Aŵa ndi asanu mwa abale angawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye anapita kwa Farao kuja ndi abale ake asanu, kukawaonetsa. Onani mutuwo |