Genesis 45:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mudzakhala m'dziko la Goseni, mudzakhala pafupi ndi ine, inu ndi ana anu, ndi ana a ana anu, ndi nkhosa zanu, ndi zoweta zanu, ndi zonse muli nazo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mudzakhala m'dziko la Goseni, mudzakhala pafupi ndi ine, inu ndi ana anu, ndi ana a ana anu, ndi nkhosa zanu, ndi zoweta zanu, ndi zonse muli nazo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mungathe kudzakhala kuno ku dziko la Goseni, kuti mukhale pafupi ndi ine. Mudzakhale kuno inuyo, ana anu, zidzukulu zanu, nkhosa zanu ndi mbuzi zomwe, ng'ombe zanu pamodzi ndi zonse zimene muli nazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo inu, ana anu, zidzukulu zanu, pamodzi ndi nkhosa ndi ngʼombe zanu ndi antchito anu amene muli nawo muzidzakhala mʼdziko la Goseni pafupi ndi ine. Onani mutuwo |