Genesis 43:4 - Buku Lopatulika4 Ngati mudzatuma mphwathu pamodzi ndi ife, tidzatsikira ndi kugulira inu chakudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ngati mudzatuma mphwathu pamodzi ndi ife, tidzatsikira ndi kugulira inu chakudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mukatilola kuti timtenge, tipita kukakugulirani chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mukalola kuti mngʼono wathuyu apite nafe, ndiye ife tidzapita kukakugulirani chakudya. Onani mutuwo |