Genesis 43:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Ejipito atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife chakudya pang'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Ejipito atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife chakudya pang'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono banja la Yakobe lija litadya tirigu yense amene adaakasuma ku Ejipito uja, Yakobe adauza ana ake aja kuti, “Pitaninso, mukatigulireko chakudya pang'ono.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsono atatha kudya tirigu yense amene anakatenga ku Igupto, Yakobo anati kwa ana ake aja, “Pitani kuti mukatigulire chakudya china pangʼono.” Onani mutuwo |