Genesis 39:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo panali zitapita izi, kuti mkazi wa mbuyake anamyang'anira maso Yosefe: ndipo mkaziyo anati, Gona ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo panali zitapita izi, kuti mkazi wa mbuyake anamyang'anira maso Yosefe: ndipo mkaziyo anati, Gona ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Patapita kanthaŵi, mkazi wa bwana wake adayamba kusirira Yosefe. Tsono mkaziyo adauza Yosefeyo kuti, “Bwanji ugone nane.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Patapita kanthawi, mkazi wa mbuye wake anayamba kusirira Yosefe nati, “Bwanji ugone nane!” Onani mutuwo |