Genesis 39:21 - Buku Lopatulika21 Koma Yehova anali ndi Yosefe namchitira iye zokoma, nampatsa ufulu pamaso pa woyang'anira kaidi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Koma Yehova anali ndi Yosefe namchitira iye zokoma, nampatsa ufulu pamaso pa woyang'anira kaidi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma Chauta anali naye Yosefe, namkomera mtima kwambiri, kotero kuti wosunga ndende adakondwera naye Yosefe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 koma Yehova anali naye, ndipo anamuonetsa kukoma mtima kwake, kotero kuti woyangʼanira ndende anakondwera ndi Yosefe. Onani mutuwo |