Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 36:34 - Buku Lopatulika

34 Ndipo Yobabu anamwalira, ndipo Husamu wa ku dziko la Atemani analamulira m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo Yobabu anamwalira, ndipo Husamu wa ku dziko la Atemani analamulira m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Yobabu atafa, Husamu wa ku dziko la Atemani adaloŵa ufumu m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Atafa Yobabu, Husamu wochokera ku dziko la Atemani, analowa mʼmalo mwake ngati mfumu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 36:34
8 Mawu Ofanana  

Ndipo ana aamuna a Elifazi ndiwo Temani, Omara, Zefo ndi Gatamu, ndi Kenazi.


Amenewa ndi mafumu a ana aamuna a Esau: ana aamuna a Elifazi woyamba wa Esau: mfumu Temani, mfumu Omara, mfumu Zefo, mfumu Kenazi,


Ndipo Bela anamwalira, ndipo Yobabu mwana wamwamuna wa Zera wa ku Bozira analamulira m'malo mwake.


Ndipo Husamu anamwalira, ndipo Hadadi mwana wamwamuna wa Bedadi, amene anakantha Midiyani m'dambo la Mowabu, analamulira m'malo mwake: dzina la mzinda wake ndi Aviti.


Namwalira Yobabu; ndi Husamu wa ku dziko la Atemani anakhala mfumu m'malo mwake.


Atamva tsono mabwenzi atatu a Yobu za choipa ichi chonse chidamgwera, anadza, yense kuchokera kwao, Elifazi wa ku Temani, ndi Bilidadi Msuki, ndi Zofari wa ku Naama, napangana kudzafika kumlirira ndi kumsangalatsa.


Za Edomu. Yehova wa makamu atero: Kodi mu Temani mulibenso nzeru? Kodi uphungu wawathera akuchenjera? Kodi nseru zao zatha psiti?


chifukwa chake atero Ambuye Yehova, Ndidzatambasulira Edomu dzanja langa, ndi kulilikhira munthu ndi nyama, ndi kulisandutsa labwinja; kuyambira ku Temani mpaka Dedani adzagwa ndi lupanga.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa