Genesis 36:2 - Buku Lopatulika2 Esau anatenga akazi ake a ana aakazi a mu Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Muhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni Muhivi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Esau anatenga akazi ake a ana akazi a m'Kanani: Ada mwana wamkazi wa Eloni Muhiti, ndi Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibiyoni Muhivi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Esau adaakwatira akazi Achikanani aŵa: Ada mwana wa Eloni Muhiti, Oholibama mwana wa Ana, mwana wa Zibiyoni Muhivi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Esau anakwatira akazi atatu a ku Kanaani. Iwowa ndiwo Ada mwana wa Eloni Mhiti; Oholibama mwana wa Ana amene anali mwana wa Zibeoni Mhivi Onani mutuwo |