Genesis 34:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Hamori atate wake wa Sekemu anatuluka kunka kwa Yakobo kukanena ndi iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Hamori atate wake wa Sekemu anatuluka kunka kwa Yakobo kukanena ndi iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Hamori, bambo wa Sekemu, adapita kukacheza ndi Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kenaka Hamori, abambo a Sekemu, anapita kukakambirana ndi Yakobo. Onani mutuwo |