Genesis 32:8 - Buku Lopatulika8 ndipo anati, Akafika Esau pa khamu limodzi nalikantha, linalo lotsala lidzapulumuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndipo anati, Akafika Esau pa khamu limodzi nalikantha, linalo lotsala lidzapulumuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mumtima mwake ankaganiza kuti, “Esau akabwera, ndipo akachita nkhondo ndi gulu loyambali, gulu linalo lingathe kuthaŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mʼmaganizo ake iye ankanena kuti, “Ngati Esau atabwera ndi kuthira nkhondo gulu limodzi, gulu lina lotsalalo likhoza kupulumuka.” Onani mutuwo |