Genesis 32:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo amithenga anabwera kwa Yakobo kuti, Tidafika kwa mbale wanu Esau, ndipo iyenso alinkudza kukomana nanu, ndipo ali nao anthu mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo amithenga anabwera kwa Yakobo kuti, Tidafika kwa mbale wanu Esau, ndipo iyenso alinkudza kukomana nanu, ndipo ali nao anthu mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Amithengawo atabwerera kwa Yakobe adati, “Tidapita kwa mbale wanu Esau, ndipo akubwera kudzakumana nanu. Ali ndi anthu 400 pamodzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pamene amithenga aja anabwerera kwa Yakobo, anati, “Tinapita kwa mʼbale wanu Esau, ndipo tsopano iye akubwera kudzakumana nanu. Ali ndi anthu 400.” Onani mutuwo |