Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 32:18 - Buku Lopatulika

18 Pomwepo uziti, Za kapolo wanu Yakobo; ndizo mphatso yotumizidwa kwa mbuyanga Esau; taonani ali pambuyo pathu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Pomwepo uziti, Za kapolo wanu Yakobo; ndizo mphatso yotumizidwa kwa mbuyanga Esau; taonani ali pambuyo pathu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Iwe ukayankhe kuti, ‘Zimenezi ndi za mtumiki wanu Yakobe, ndipo akuzitumiza kwa inu mbuyake, kuti zikhale mphatso. Yakobe mwiniwake ali m'mbuyo mwathumu.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Pamenepo ukayankhe kuti, ‘Zimenezi ndi za wantchito wanu, Yakobo, ndipo wazipereka kwa inu, Esau, mbuye wake ngati mphatso. Mtumiki wanuyu akubwera mʼmbuyo mwathumu.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 32:18
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anauza wotsogolera kuti, Pamene akomana nawe mkulu wanga Esau ndi kufunsa iwe kuti, Ndiwe yani, umuka kuti? Za yani zimenezi patsogolo pako?


Ndipo anauzanso wachiwiri ndi wachitatu, ndi onse anatsata magulu, kuti, Muzinena kwa Esau chotero, pamene mukomana naye:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa