Genesis 32:15 - Buku Lopatulika15 ngamira zamkaka makumi atatu ndi ana ao, ng'ombe zazikazi makumi anai, zazimuna khumi, abulu aakazi makumi awiri ndi ana khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ngamira zamkaka makumi atatu ndi ana ao, ng'ombe zazikazi makumi anai, zazimuna khumi, abulu akazi makumi awiri ndi ana khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 ngamira zamkaka makumi atatu pamodzi ndi ana ake, ng'ombe zazikazi makumi anai, ndi zazimuna khumi, ndi abulu aakazi makumi aŵiri ndi amphongo khumi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 ngamira za mkaka 30 ndi ana awo, ngʼombe zazikazi 40 ndi zazimuna khumi, ndipo abulu aakazi makumi awiri ndi abulu aamuna khumi. Onani mutuwo |