Genesis 27:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Isaki atate wake anati kwa iye, Senderatu, undimpsompsone mwana wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Isaki atate wake anati kwa iye, Senderatu, undimpsompsone mwana wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Tsono bambo wakeyo adati, “Bwera pafupi, udzandimpsompsone, mwana wanga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Tsono Isake anati kwa Yakobo, “Bwera kuno mwana wanga undipsompsone.” Onani mutuwo |