Genesis 26:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anakumbanso chitsime china, ndipo anakangana nachonso; natcha dzina lake Sitina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anakumbanso chitsime china, ndipo anakangana nachonso; natcha dzina lake Sitina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Antchito a Isaki aja adakumba chitsime china, ndipo padaukanso mkangano wina pa za chitsime chimenecho. Motero adachitcha Chidani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kenaka iwo anakumba chitsime china, koma anakangananso chifukwa cha chitsimecho. Choncho anachitcha dzina lakuti Chidani. Onani mutuwo |