Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 26:19 - Buku Lopatulika

19 Ndipo anyamata a Isaki anakumba m'chigwa, napeza kumeneko chitsime cha madzi otumphuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Ndipo anyamata a Isaki anakumba m'chigwa, napeza kumeneko chitsime cha madzi otumphuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Antchito a Isaki adakumba chitsime m'chigwa, napezamo madzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Antchito a Isake anakumba mʼchigwamo ndipo anapezamo kasupe wa madzi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 26:19
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Isaki anafukulanso zitsime za madzi, anazikumba masiku a Abrahamu atate wake; chifukwa kuti Afilisti anazitseka atafa Abrahamu: ndipo anazitcha maina monga maina omwe anazitcha atate wake.


Ndipo abusa a Gerari anakangana ndi abusa a Isaki kuti, Madzi ndi athu; ndipo anatcha dzina la chitsimecho Eseke: chifukwa anakangana naye.


Ndiwe kasupe wa m'minda, chitsime cha madzi amoyo, ndi mitsinje yoyenda yochokera ku Lebanoni.


Iye wokhulupirira Ine, monga chilembo chinati, Mitsinje ya madzi amoyo idzayenda, kutuluka m'kati mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa