Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 24:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo mnyamatayo anaika dzanja lake pansi pa ntchafu yake ya Abrahamu Mbuye wake, namlumbirira iye za chinthucho.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo mnyamatayo anaika dzanja lake pansi pa ntchafu yake ya Abrahamu Mbuye wake, namlumbirira iye za chinthucho.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Motero wantchitoyo adaika dzanja lake m'kati mwa ntchafu za Abrahamu mbuye wake, ndipo adalumbira kuti, “Ndidzachita zonse zimene mwanenazi.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Choncho wantchitoyo anayika dzanja lake pansi pa ntchafu ya mbuye wake Abrahamu nalumbira kwa iye kuti adzachitadi monga mwa mawu a Abrahamu.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:9
2 Mawu Ofanana  

Ndipo mnyamatayo anatenga ngamira khumi za mbuyake, namuka: chifukwa kuti chuma chonse cha mbuyake chinali m'dzanja lake: ndipo anachoka namuka ku Mesopotamiya, kumzinda wa Nahori.


Ndipo Abrahamu anati kwa mnyamata wake wamkulu wa pa nyumba yake, amene analamulira pa zonse anali nazo, Taikatu dzanja lako pansi pa ntchafu yanga:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa