Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 24:55 - Buku Lopatulika

55 Ndipo mlongo wake ndi amake anati, Namwali akhale ndi ife masiku akuwerengeka, afikire khumi; patsogolo pake iye adzamuka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

55 Ndipo mlongo wake ndi amake anati, Namwali akhale ndi ife masiku akuwerengeka, afikire khumi; patsogolo pake iye adzamuka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

55 Koma mai wake wa Rebeka, pamodzi ndi mlongo wakeyo, adati, “Ai, namwaliyu akhale ndi ife kuno kanthaŵi, osachepera masiku khumi, pambuyo pake ndiye adzapite.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

55 Koma mlongo wake ndi amayi ake a Rebeka anayankha kuti, “Muloleni mtsikanayu abakhala nafe masiku khumi kapena kupyolerapo, kenaka mukhoza kupita.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 24:55
5 Mawu Ofanana  

Ndipo iye anati kwa iwo, Musandichedwetse ine, pakuti Yehova wandiyendetsa bwino m'njira yanga: mundilole ine ndinke kwa mbuyanga.


Ndipo panali atapita masiku, Kaini anatenga zipatso za nthaka, nsembe ya kwa Yehova.


Munthu akagulitsa nyumba yogonamo, m'mzinda wa m'linga, aiombole chisanathe chaka choigulitsa; kufikira kutha chaka akhoza kuombola.


Atapita masiku ndipo anabweranso kudzamtenga, napatuka iye kukaona mtembo wa mkango; ndipo taona, m'chitanda cha mkango munali njuchi zoundana, ndi uchi.


Ndipo mpongozi wake, ndiye atate wa mkaziyo, anamuimika kuti akhale naye masiku atatu; nadya namwa nagona komweko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa