Genesis 21:18 - Buku Lopatulika18 Tauka, nuukitse mnyamatayo, ndi kumgwira m'dzanja lako; chifukwa ndidzamuyesa iye mtundu waukulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Tauka, nuukitse mnyamatayo, ndi kumgwira m'dzanja lako; chifukwa ndidzamuyesa iye mtundu waukulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Dzuka, pita, ukamnyamule ndi kumgwiritsa ndi dzanja lako. Zidzukulu zako zidzakhala mtundu waukulu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Munyamule mnyamatayo ndipo umugwire dzanja pakuti ndidzamupanga kukhala mtundu waukulu.” Onani mutuwo |