Genesis 20:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Abimeleki anati, Taona dziko langa lili pamaso pako; kumene kuli kwabwino pamaso pako takhala kumeneko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Abimeleki anati, Taona dziko langa lili pamaso pako; kumene kuli kwabwino pamaso pako takhala kumeneko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Adauza Abrahamu kuti, “Dziko lonseli ndi langa, ungathe kukhala kulikonse komwe ukufuna.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Tsono Abimeleki anati kwa Abrahamu, “Dziko langa ndi limene ukulionali; ukhale paliponse pamene ufuna.” Onani mutuwo |