Genesis 20:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Unaona chiyani iwe kuti wachita ichi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Abimeleki anati kwa Abrahamu, Unaona chiyani iwe kuti wachita ichi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Chifukwa chiyani wachita zimenezi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo Abrahamu anafunsa Abimeleki kuti, “Chifukwa chiyani wachita zimenezi?” Onani mutuwo |