Genesis 2:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yehova Mulungu anabzala m'munda ku Edeni chakum'mawa; momwemo ndipo adaika munthu adamuumbayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yehova Mulungu anabzala m'munda ku Edeni chakum'mawa; momwemo ndipo adaika munthu adamuumbayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kenaka Chauta adatsekula munda mu Edeni chakuvuma, ndipo munthu adamuumbayo adamkhazika m'menemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kenaka Yehova Mulungu anatsekula munda wa Edeni chakummawa; kumeneko anayikako munthu amene anamupanga uja. Onani mutuwo |