Genesis 19:4 - Buku Lopatulika4 Koma asanagone, anthu a m'mzindamo anthu a Sodomu, anazinga nyumba, anyamata ndi okalamba, anthu onse a m'mbali zonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma asanagone, anthu a m'mudzimo anthu a Sodomu, anazinga nyumba, anyamata ndi okalamba, anthu onse a m'mbali zonse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Alendowo asanakagone, anthu onse amumzindamo, achinyamata ndi okalamba omwe, adadzazinga nyumbayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Alendo aja asanapite kogona, amuna onse achinyamata ndi achikulire ochokera mbali zonse za mzinda wa Sodomu anazinga nyumba ya Loti. Onani mutuwo |