Genesis 19:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo ana aakazi awiri a Loti anali ndi pakati pa atate wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo ana akazi awiri a Loti anali ndi pakati pa atate wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Mwa njira imeneyi, ana onse aŵiriwo a Loti adatenga pathupi pa bambo wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Choncho ana onse awiri a Loti aja anatenga pathupi pa abambo awo. Onani mutuwo |