Genesis 18:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo anati Yehova, Ndikapeza mu Sodomu olungama makumi asanu m'kati mwa mzinda, ndidzasiya malo onse chifukwa cha iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo anati Yehova, Ndikapeza m'Sodomu olungama makumi asanu m'kati mwa mudzi, ndidzasiya malo onse chifukwa cha iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Chauta adayankha kuti, “Ndikapeza anthu 50 osachimwa m'Sodomu, ndidzauleka mzinda wonsewo osauwononga, chifukwa cha anthu 50 amenewo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Yehova anati, “Nditapeza anthu makumi asanu olungama mu mzinda wa Sodomu, ndidzasiya malo onsewo osawawononga chifukwa cha iwo.” Onani mutuwo |