Genesis 17:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Abrahamu anati kwa Mulungu, Ha! Ismaele akhale ndi moyo pamaso panu! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Abrahamu anati kwa Mulungu, Ha! Ismaele akhale ndi moyo pamaso panu! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndipo adauza Mulungu kuti, “Ndikukupemphani kuti mungodalitsa Ismaele yemweyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo Abrahamu anati kwa Mulungu, “Bwanji mumudalitse Ismaeli.” Onani mutuwo |