Genesis 16:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Sarai mkazi wake wa Abramu sanambalire iye mwana; ndipo anali ndi mdzakazi, wa ku Ejipito, dzina lake Hagara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Sarai mkazi wake wa Abramu sanambalire iye mwana; ndipo anali ndi mdzakazi, wa ku Ejipito, dzina lake Hagara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Sarai mkazi wa Abramu, sadam'balire ana Abramuyo. Koma Sarai anali ndi mdzakazi wake wa ku Ejipito dzina lake Hagara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsono Sarai, mkazi wa Abramu anali asanamuberekere ana Abramuyo. Koma anali ndi wantchito wamkazi wa ku Igupto dzina lake Hagara; Onani mutuwo |