Genesis 15:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Abramu anati, Taonani, simunandipatse ine mbeu; ndipo, taonani, wobadwa m'nyumba mwanga adzalowa m'malo mwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Abramu anati, Taonani, simunandipatse ine mbeu; ndipo, taonani, wobadwa m'nyumba mwanga adzalowa m'malo mwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Simudandipatse ana, motero mmodzi mwa akapolo anga ndiye amene adzalandire chuma changa kuti chikhale choloŵa chake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Inu simunandipatse ana kotero kuti wantchito wa ku nyumba kwanga ndiye amene adzalowe mʼmalo mwanga.” Onani mutuwo |