Genesis 14:24 - Buku Lopatulika24 koma chokhachi anadya anyamata, ndi gawo lao la anthu amene ananka pamodzi ndi ine, Anere, Esikolo, ndi Mamure, iwo atenge gawo lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 koma chokhachi anadya anyamata, ndi gawo lao la anthu amene ananka pamodzi ndi ine, Anere, Esikolo, ndi Mamure, iwo atenge gawo lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Sinditenga kalikonse ai. Nditengako zokhazo zimene anyamata anga adadya, ndi zoyenera kugaŵira amene adandiperekeza, monga Anere, Esikolo ndi Mamure. Iwo atengeko magawo ao.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Sindidzalandira kanthu kalikonse kupatula zokhazo zimene anthu anga adya ndi gawo la katundu la anthu amene ndinapita nawo monga Aneri, Esikolo ndi Mamre. Iwowa atenge gawo lawo.” Onani mutuwo |