Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 12:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo Farao analamulira anthu ake za iye; ndipo anamperekeza iye m'njira ndi mkazi wake ndi zonse anali nazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo Farao analamulira anthu ake za iye; ndipo anamperekeza iye m'njira ndi mkazi wake ndi zonse anali nazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Farao adalamula anthu ake, ndipo iwowo adatulutsa Abramu ndi mkazi wake m'dzikomo, pamodzi ndi zonse zimene anali nazo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Farao analamula asilikali ake ndipo iwo anamutulutsa Abramu pamodzi ndi mkazi wake ndi zonse anali nazo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 12:20
6 Mawu Ofanana  

Chifukwa chanji unati, Ndiye mlongo wanga? Kotero ndinamtenga iye akhale mkazi wanga; tsopano suyu mkazi wako; mtenge nuchoke.


Ndipo anakwera Abramu kuchoka ku Ejipito, iye ndi mkazi wake, ndi zonse anali nazo, ndi Loti pamodzi naye, kunka ku dziko la kumwera.


Ndipo Mose analola mpongozi wake amuke; ndipo anachoka kunka ku dziko lake.


Mtima wa mfumu uli m'dzanja la Yehova ngati mitsinje ya madzi; aulozetsa komwe afuna.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa