Genesis 11:32 - Buku Lopatulika32 Masiku a Tera anali zaka mazana awiri kudza zisanu; ndipo anafa Tera mu Harani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Masiku a Tera anali zaka mazana awiri kudza zisanu; ndipo anafa Tera m'Harani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Ndipo Tera adafera kumeneko ali wa zaka 205. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Tera anamwalira ku Harani ali ndi zaka 205. Onani mutuwo |