Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 11:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo anafa Harani pamaso pa atate wake Tera m'dziko la kubadwa kwake, mu Uri wa kwa Akaldeya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo anafa Harani pamaso pa atate wake Tera m'dziko la kubadwa kwake, m'Uri wa kwa Akaldeya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Haraniyo adafera m'mudzi wa kwao dzina lake Uri, wa ku Kaldeya. Adafa atate ake akali moyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Abambo ake a Tera akanali ndi moyo, Harani anamwalira ku Uri wa ku Akaldeya kumene anabadwira.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 11:28
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Tera anatenga Abramu mwana wake wamwamuna, ndi Loti mwana wa Harani, mwana wake wamwamuna, ndi Sarai mpongozi wake, mkazi wa mwana wake Abramu; ndipo anatuluka pamodzi nao ku Uri wa kwa Akaldeya kuti amuke ku dziko la Kanani, ndipo anafika ku Harani, nakhala kumeneko.


Ndipo anati kwa iye, Ine ndine Yehova amene ndinatulutsa iwe mu Uri wa kwa Akaldeya, kuti ndikupatse iwe dziko limeneli likhale lakolako.


Inu ndinu Yehova Mulungu amene munasankha Abramu ndi kumtulutsa mu Uri wa kwa Akaldeya, ndi kumutcha dzina lake Abrahamu;


Akali chilankhulire uyu, anadza winanso, nati, Ababiloni anadzigawa magulu atatu, nazigwera ngamira, nazitenga, nawapha anyamata ndi lupanga lakuthwa, ndipo ndapulumuka ine ndekha kudzakuuzani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa