Genesis 1:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lachitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ndipo kudali madzulo ndiponso m'maŵa, tsiku lachitatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndipo panali madzulo ndiponso mmawa pa tsiku lachitatu. Onani mutuwo |