Eksodo 9:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako kuthambo, kuti pakhale matalala padziko lonse la Ejipito, pa anthu ndi pa zoweta, ndi pa zitsamba zonse zakuthengo, m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Tambasula dzanja lako kuthambo, kuti pakhale matalala pa dziko lonse la Ejipito, pa anthu ndi pa zoweta, ndi pa zitsamba zonse za kuthengo, m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono Chauta adauza Mose kuti, “Kweza dzanja lako kumwamba, ndipo matalala adzagwa pa anthu, pa nyama, ndi pa zomera zonse zam'minda, m'dziko lonse la Ejipito.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kenaka Yehova anati kwa Mose, “Kweza dzanja lako kumwamba kuti matalala agwe pa dziko lonse la Igupto, pa munthu aliyense, pa ziweto ndi pa zonse zomera mʼminda ya Igupto.” Onani mutuwo |