Eksodo 9:20 - Buku Lopatulika20 Iyeyu wa anyamata a Farao wakuopa mau a Yehova anathawitsira m'zinyumba anyamata ake ndi zoweta zake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Iyeyu wa anyamata a Farao wakuopa mau a Yehova anathawitsira m'zinyumba anyamata ake ndi zoweta zake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Nduna zina za Farao zidachita mantha chifukwa cha mau amene adanena Chauta, ndipo zidatsekera akapolo ao m'nyumba pamodzi ndi zoŵeta zao zomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Nduna za Farao zinachita mantha ndi mawu a Yehova, ndipo zinalowetsa antchito awo ndi ziweto zawo mʼnyumba. Onani mutuwo |