Eksodo 8:15 - Buku Lopatulika15 Koma pamene Farao anaona kuti panali kupuma, anaumitsa mtima wake, osamvera iwo; monga adalankhula Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma pamene Farao anaona kuti panali kupuma, anaumitsa mtima wake, osamvera iwo; monga adalankhula Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Farao ataona kuti zinthu zayamba kukhala bwino, adaumitsa mtima wake, ndipo sadafunenso kumvera Mose ndi Aroni monga momwe Chauta adaanenera muja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Koma Farao ataona kuti zinthu zinayambanso kukhala bwino, anawumitsanso mtima wake ndipo sanamverenso mawu a Mose ndi Aaroni, monga momwe Yehova ananenera. Onani mutuwo |