Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 5:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo potuluka kwa Farao iwo anakomana ndi Mose ndi Aroni, alikuima popenyana nao;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo potuluka kwa Farao iwo anakomana ndi Mose ndi Aroni, alikuima popenyana nao;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Tsono atachoka kwa Farao kuja, adakumana ndi Mose ndi Aroni amene ankaŵadikira,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Atachoka pamaso pa Farao, anakumana ndi Mose ndi Aaroni akuwadikira,

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 5:20
2 Mawu Ofanana  

Ndipo akapitao a ana a Israele anaona kuti kudawaipira, pamene ananena, Musamachepetsa njerwa zanu, ntchito ya tsiku pa tsiku lake.


ndipo ananena nao, Yehova akupenyeni, naweruze; pakuti mwatinyansitsa pamaso pa Farao, ndi pamaso pa anyamata ake, ndi kuwapatsa lupanga m'dzanja lao kutipha nalo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa