Eksodo 39:40 - Buku Lopatulika40 nsalu zotchingira za pabwalo, nsichi zake, ndi makamwa ake, ndi nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo, zingwe zake, ndi zichiri zake, ndi zipangizo zonse za ntchito ya Kachisi, za ku chihema chokomanako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 nsalu zochingira za pabwalo, nsichi zake, ndi makamwa ake, ndi nsalu yotsekera pa chipata cha pabwalo, zingwe zake, ndi zichiri zake, ndi zipangizo zonse za ntchito ya Kachisi, za ku chihema chokomanako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Adabweranso ndi nsalu zochingira bwalo pamodzi ndi nsanamira zake ndi masinde ake, nsalu yochingira pa chipata choloŵera m'bwalolo, pamodzi ndi zingwe zake ndi zikhomo zake, ndiponso zipangizo zonse zotumikira nazo m'chihema cha Chauta chija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 nsalu yotchingira bwalo pamodzi ndi mizati yake ndi matsinde ake ndiponso nsalu yotchingira pa khomo lolowera ku bwalo; zingwe zake ndi zikhomo za tenti; zipangizo zonse za chihema, tenti ya msonkhano; Onani mutuwo |