Eksodo 39:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo anaomba malaya a bafuta, a ntchito yoomba, a Aroni, ndi a ana ake aamuna, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo anaomba malaya a bafuta, a ntchito yoomba, a Aroni, ndi a ana ake amuna, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Tsono Aroni ndi ana ake, amisiri aja adaŵapangira miinjiro, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Kwa Aaroni ndi ana ake anawapangira minjiro ya nsalu yofewa yosalala, yolukidwa bwino ndi munthu waluso, Onani mutuwo |