Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 39:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo anaomba efodi wa golide, lamadzi, lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo anaomba efodi wa golide, lamadzi, lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Adapanga chovala chopatulika cha efodi ndi nsalu yagolide ndiponso ndi nsalu yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndi ya bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Popanga efodi, iwo anagwiritsa ntchito golide, nsalu yamtundu wa mtambo, yapepo, yofiira, yosalala yofewa.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 39:2
6 Mawu Ofanana  

Mwana wamkazi wa mfumu ngwa ulemerero wonse m'kati mwa nyumba, zovala zake nza malukidwe agolide.


ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;


miyala yaberulo, ndi miyala yoika paefodi, ndi pachapachifuwa.


Ndipo anasula golide waphanthiphanthi, nalemba nsambo, kuti amuombe pamodzi ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ntchito ya m'misiri.


Ndipo anamveka ndi malaya a m'kati, nammanga m'chuuno ndi mpango, namveka ndi mwinjiro, namveka ndi efodi, nammanga m'chuuno ndi mpango wa efodi nammanga nao pathupi pake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa