Eksodo 38:31 - Buku Lopatulika31 ndi makamwa a pabwalo pozungulira, ndi makamwa a ku chipata cha pabwalo, ndi zichiri zonse za chihema, ndi zichiri zonse za pabwalo pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 ndi makamwa a pabwalo pozungulira, ndi makamwa a ku chipata cha pabwalo, ndi zichiri zonse za chihema, ndi zichiri zonse za pabwalo pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 masinde a bwalo lonse lozungulira, ndi zikhomo zonse za chihema cha Chauta ndi za bwalo lonse lozungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 matsinde ozungulira bwalo ndiponso a pa chipata pake, ndi zikhomo zonse za tentiyo ndi matsinde a malo wozungulirapo. Onani mutuwo |